Mulungu amamva zambiri kuposa pemphero langa, Iye amaona chokhumba cha mtima wanga. Kodi Iye ayenera kuona chiyani mumtima mwanga kuti andiyankhe mapemphero anga
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
"Pemphero ndi limodzi mwa mizati yaikulu m'moyo wanga. Ndine wokondwa kwambiri kuti ndikhoza kupita kwa Mulungu ndi kupeza thandizo. Kumbi ndingachita wuli asani ndisoŵa?"
Kodi mumapemphera m'njira imene Baibulo limanena kuti muyenera kupemphera?
Yesu anaphunzitsa ophunzira Ake zimene zinali zofunika kwambiri kupempherera.
Mu kukhumudwa kwanga ndi mkwiyo wanga za dziko limene ndimakhala, ndinapeza vumbulutso lofunika: kwenikweni ndi udindo wanga kupempherera dziko langa.
Estere anali "msilikali wa pemphero", mkazi woopa Mulungu wokhala ndi mgwirizano wolimba waumwini ndi Yesu.
N'chifukwa chiyani pemphero ndi lofunika kwambiri kwa wokhulupirira?