Kodi muli ndi chiyembekezo cha moyo wosatha? Kodi mungakhale ndi moyo umene umatsogolera ku moyo wosatha m'nthaŵi yanu pano padziko lapansi?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Tilibe mayankho onse okhudza nthawi zomaliza. Koma kodi mukudziwa chinthu chofunika kwambiri chimene mungachite kuti mukonzekere?
Kukhala wokhoza kuyembekezera tsiku limene ndidzakumana ndi Mpulumutsi wanga ndi kulandira mphotho ya moyo wokhulupirika, ndi imodzi mwa mapindu aakulu koposa a kukhala Mkristu.