Kodi timagwiritsa bwanji ntchito nthawi yathu padziko pano?
Umboni wa Paulo unali wakuti: “Ndamenya nkhondo yabwino, ndatsiriza bwino mpikisano wa liwiro ndipo ndasunga chikhulupiriro.” Kodi umboni wako udzakhala wotani?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita