Tsopano mwakonzeka kuyamba moyo watsopano wonse!
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Kodi munayamba mwaganizapo kapena kunena mawu amenewa? Kodi mukudziwa zimene Mulungu anauza Yeremiya pamene ananena zimenezi?
Pamene Yesu anaukitsidwa kwa akufa ndipo Mzimu Woyera anabwera, anapereka chiyembekezo kwa ophunzira Ake onse – kuphatikizapo inu ndi ine! Werengani zambiri!
Kodi mwawerengera mtengo wake?
Pali kusiyana kwakukulu pakati pa anthu odzitcha Akhristu. Ndi angati tinganene kuti akulemekezadi Mulungu ndi moyo umene akukhala?