Ngati Kristu anabweradi m'thupi, m'chibadwa cha munthu, kodi chinali chibadwa chotani? N'chifukwa chiyani zimenezi zili zofunika?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Kodi mukudziwa kuti pa chilichonse chimene timachita, anthu adzaona moyo wa Khristu kapena moyo wa Satana mwa ife?
Ndife anthu. Timachimwa. Kodi ndi mapeto a nkhaniyi?