Kodi kumvera n'kofunika bwanji pankhani ya chikhulupiriro chathu?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Mawu awa a Yesu anali maziko a ntchito Yake yonse ya chipulumutso! Kodi Iye anachita chiyani, ndipo zikutanthauzanji kwa ife?
Zingakhale zovuta kumvetsa kuti pamene Mulungu atilanga ndi kutiwongolera, kwenikweni ndi chisomo Chake.
Ngati Kristu anabweradi m'thupi, m'chibadwa cha munthu, kodi chinali chibadwa chotani? N'chifukwa chiyani zimenezi zili zofunika?
Kodi mukudziwa kuti pa chilichonse chimene timachita, anthu adzaona moyo wa Khristu kapena moyo wa Satana mwa ife?
Kodi ndingayende bwanji mwa Mzimu?
Ndingaone kuti ndimakhala wodetsedwa ndikayesedwa. Koma kodi ndinachimwa?
Debora anali mneneri wamkazi ndi woweruza mu Israyeli. Iye ali chitsanzo champhamvu cha mmene chikhulupiriro m'zochita chimagwirira ntchito!
Cholinga cha Satana ndicho kutilekanitsa ndi Mulungu. Umu ndi mmene tingamuletsere.