Zapadziko lapansi

Amatanthauza chilichonse cha dziko lapansi, mosiyana ndi zakumwamba. Chitsanzo: Chuma chapadziko lapansi/Chuma chakumwamba. Zapadziko lapansi zipita (ndi zanthawi), koma zakumwamba nzosatha. ( Mateyu 6:19-21; Akolose 3:2; 1 Yohane 2:17 )