Ophunzila

Wophunzira ndi dzina lina la wotsatira Kristu, amene akuphunzira kukhala ngati Mbuye wake.Monga wophunzira mumatsatira Yesu Khristu, yemwe ali Mbuye ndipo pakukhala ngati Iye mumafanana naye kwambiri. ( Mateyu 16:24; 1 Petro 2:21-22 )