Munthu wamkati

Munthu wakunja ndi thupi lathu pamene tili padziko lapansi pano. Munthu wathu wamkati ndiye mzimu wathu wamuyaya ndi moyo wathu. ( Aroma 7:22; 2 Akorinto 4:16; Aefeso 3:16; Mateyu 10:28 )