Kuchita uchimo

Kuchita uchimo ndi kupanga chinthu chimene iweyo ukudziwa kuti ndizotsutsana ndi chifuniro cha Mulungu ndi malamulo ake.Ndi pamene muyesedwa ndi zilakolako zomwe zili mwa inu, ndipo mukuvomereza kuchitapo kanthu pa mayeserowo, podziwa bwino kuti Mulungu sakondwera nawo. "Kuchita" kumeneku kungachitike m'mawu, zochita, kapena malingaliro. ( Yakobo 1:14-15 )